Salimo 109:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Alekeni anditemberere,+Koma inu mundipatse madalitso.+Iwo aimirira kuti andiukire koma inu muwachititse manyazi,+Ndipo ine mtumiki wanu ndisangalale.+
28 Alekeni anditemberere,+Koma inu mundipatse madalitso.+Iwo aimirira kuti andiukire koma inu muwachititse manyazi,+Ndipo ine mtumiki wanu ndisangalale.+