Oweruza 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zili choncho, Hiberi+ Mkeni anapatukana ndi Akeni,+ ana a Hobabu mpongozi wa Mose,+ ndipo anamanga hema wake pafupi ndi mtengo waukulu ku Zaananimu, ku Kedesi.
11 Zili choncho, Hiberi+ Mkeni anapatukana ndi Akeni,+ ana a Hobabu mpongozi wa Mose,+ ndipo anamanga hema wake pafupi ndi mtengo waukulu ku Zaananimu, ku Kedesi.