Genesis 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Mulungu wandipatsa mphoto chifukwa ndapereka kapolo wanga kwa mwamuna wanga.” Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Isakara.*+ Genesis 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Isakara+ ndi bulu wa mafupa olimba, amagona pansi atasenza matumba a katundu uku ndi uku.
18 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Mulungu wandipatsa mphoto chifukwa ndapereka kapolo wanga kwa mwamuna wanga.” Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Isakara.*+