Ekisodo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa tsiku lotsatira, Mose anati kwa anthuwo: “Inuyo mwachita tchimo lalikulu.+ Choncho ndikwera kupita kwa Yehova kuti mwina ndikakam’chonderera angakukhululukireni tchimo lanu.”+
30 Pa tsiku lotsatira, Mose anati kwa anthuwo: “Inuyo mwachita tchimo lalikulu.+ Choncho ndikwera kupita kwa Yehova kuti mwina ndikakam’chonderera angakukhululukireni tchimo lanu.”+