Deuteronomo 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anamuonetsa Negebu+ ndi Chigawo*+ cha Yorodano, chigwa cha ku Yeriko, mzinda wa mitengo ya kanjedza,+ mpaka ku Zowari.+ Yoswa 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha ana a Isiraeli. Palibe amene anali kutuluka kapena kulowa mumzindawo.+
3 Anamuonetsa Negebu+ ndi Chigawo*+ cha Yorodano, chigwa cha ku Yeriko, mzinda wa mitengo ya kanjedza,+ mpaka ku Zowari.+
6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha ana a Isiraeli. Palibe amene anali kutuluka kapena kulowa mumzindawo.+