Numeri 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno panabuka moto wochokera kwa Yehova,+ umene unapsereza amuna 250 omwe anali kupereka nsembe zofukiza+ aja. Salimo 106:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Moto unayaka pakati pa msonkhano wawo.+Malawi amoto ananyeketsa anthu oipawo.+
35 Ndiyeno panabuka moto wochokera kwa Yehova,+ umene unapsereza amuna 250 omwe anali kupereka nsembe zofukiza+ aja.