41 Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana aamuna onse oyamba kubadwa a Isiraeli.+ Unditengerenso ziweto zonse za Alevi m’malo mwa ziweto zonse zoyamba kubadwa za ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova.”
45 “Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana onse aamuna oyamba kubadwa a Isiraeli. Unditengerenso ziweto za Alevi zikhale zanga m’malo mwa ziweto za Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova.