Genesis 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anakhala munthu woipa pamaso pa Yehova.+ Chotero Yehova anamupha.+ Genesis 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Onani anadziwa kuti anawo sadzakhala ake.+ Choncho, nthawi zonse akagona ndi mkazi wa m’bale wakeyo, anali kutaya pansi umuna wake kuti asam’berekere ana m’bale wakeyo.+ Genesis 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zimene anachitazo zinamuipira Yehova,+ chotero nayenso anamupha.+
7 Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anakhala munthu woipa pamaso pa Yehova.+ Chotero Yehova anamupha.+
9 Koma Onani anadziwa kuti anawo sadzakhala ake.+ Choncho, nthawi zonse akagona ndi mkazi wa m’bale wakeyo, anali kutaya pansi umuna wake kuti asam’berekere ana m’bale wakeyo.+