Genesis 38:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pambuyo pake, m’bale wake yemwe anali ndi kachingwe kofiira kwambiri padzanja lake uja anatuluka, ndipo anamutcha dzina lakuti Zera.+ 1 Mbiri 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamara+ mpongozi wake ndiye anam’berekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda anali asanu.
30 Pambuyo pake, m’bale wake yemwe anali ndi kachingwe kofiira kwambiri padzanja lake uja anatuluka, ndipo anamutcha dzina lakuti Zera.+