Genesis 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+
20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+