3 Tselofekadi+ mwana wa Heferi, mwana wa Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, analibe ana aamuna, koma anali ndi ana aakazi. Mayina a anawo anali: Mala, Nowa, Hogila, Milika, ndi Tiriza.+
15 Makiri anapezera akazi Hupimu ndi Supimu, ndipo dzina la mlongo wake linali Maaka.) Mwana wake wachiwiri dzina lake linali Tselofekadi,+ koma Tselofekadi anali ndi ana aakazi okhaokha.+