Genesis 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anapitiriza kuwadalitsa pa tsikulo.+ Anati: “Pogwiritsa ntchito dzina lako, Aisiraeli azidzadalitsana kuti,‘Mulungu akudalitse monga anadalitsira Efuraimu ndi Manase.’”+ Choncho Isiraeli anaikabe Efuraimu patsogolo pa Manase.+ Yoswa 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Poyankha, Yoswa anauza anthu a fuko la Yosefe, omwe ndi Efuraimu ndi Manase, kuti: “Ndinu anthu ochuluka, ndipo ndinu amphamvu kwambiri.+ Simuyenera kukhala ndi gawo limodzi lokha,+
20 Iye anapitiriza kuwadalitsa pa tsikulo.+ Anati: “Pogwiritsa ntchito dzina lako, Aisiraeli azidzadalitsana kuti,‘Mulungu akudalitse monga anadalitsira Efuraimu ndi Manase.’”+ Choncho Isiraeli anaikabe Efuraimu patsogolo pa Manase.+
17 Poyankha, Yoswa anauza anthu a fuko la Yosefe, omwe ndi Efuraimu ndi Manase, kuti: “Ndinu anthu ochuluka, ndipo ndinu amphamvu kwambiri.+ Simuyenera kukhala ndi gawo limodzi lokha,+