Numeri 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwa ana a Kohati, panali banja la Aamuramu, banja la Aizara, banja la Aheburoni ndi banja la Auziyeli. Awa ndiwo anali mabanja a Akohati.+ 1 Mbiri 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana a Kohati anali Amuramu,+ Izara,+ Heburoni,+ ndi Uziyeli.+
27 Mwa ana a Kohati, panali banja la Aamuramu, banja la Aizara, banja la Aheburoni ndi banja la Auziyeli. Awa ndiwo anali mabanja a Akohati.+