Levitiko 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atatero, moto unatsika kuchokera kwa Yehova ndi kuwawononga,+ moti anafa pamaso pa Yehova.+ Numeri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova pamene anapereka kwa Yehova moto wosaloleka+ m’chipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Komabe, Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo. 1 Mbiri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nadabu ndi Abihu+ anamwalira opanda ana aamuna bambo awo akali ndi moyo,+ koma Eleazara+ ndi Itamara anapitiriza kukhala ansembe.
4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova pamene anapereka kwa Yehova moto wosaloleka+ m’chipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Komabe, Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo.
2 Nadabu ndi Abihu+ anamwalira opanda ana aamuna bambo awo akali ndi moyo,+ koma Eleazara+ ndi Itamara anapitiriza kukhala ansembe.