Genesis 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+ Genesis 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+
20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+
13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+