Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 28:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pang’ombe iliyonse yamphongo, muzipereka ufa wosalala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa, monga nsembe yake yambewu.+ Ufawo uzikhala wothira mafuta. Nkhosa yamphongo imodziyo+ muziipereka limodzi ndi nsembe yambewu ya ufa wosalala wokwana magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa. Ufawo uzikhala wothira mafuta.

  • Numeri 29:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Muziperekanso ufa wosalala wothira mafuta monga nsembe zake zambewu. Ufawo uzikhala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa pang’ombe yamphongoyo, magawo awiri mwa magawo 10 pankhosa yamphongoyo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena