Numeri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+ Numeri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzipereka nsembezi limodzi ndi ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,+ monga nsembe yambewu.+ Ufawo muziuthira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.+ Numeri 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muziipereka pamodzi ndi nsembe yachakumwa+ chokwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Pa mwana wa nkhosa wamphongo+ aliyense muzipereka nsembe yachakumwa. Muzithirira Yehova nsembe yachakumwa choledzeretsayo+ m’malo oyera.
3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+
5 Muzipereka nsembezi limodzi ndi ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,+ monga nsembe yambewu.+ Ufawo muziuthira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.+
7 Muziipereka pamodzi ndi nsembe yachakumwa+ chokwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Pa mwana wa nkhosa wamphongo+ aliyense muzipereka nsembe yachakumwa. Muzithirira Yehova nsembe yachakumwa choledzeretsayo+ m’malo oyera.