Levitiko 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kapena ngati wauzidwa kuti wachimwa mwa kuphwanya lamulo,+ azibweretsa mbuzi yaing’ono yamphongo,+ yopanda chilema, kuti ikhale nsembe yake. Numeri 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muziperekanso mwana wa mbuzi+ monga nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+
23 kapena ngati wauzidwa kuti wachimwa mwa kuphwanya lamulo,+ azibweretsa mbuzi yaing’ono yamphongo,+ yopanda chilema, kuti ikhale nsembe yake.
15 Muziperekanso mwana wa mbuzi+ monga nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+