Levitiko 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musagwire ntchito iliyonse yolemetsa.
36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musagwire ntchito iliyonse yolemetsa.