Levitiko 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ngati akupereka lonjezo+ monga nsembe yake kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo angathenso kudya imene yatsala pa tsiku lotsatira. Levitiko 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake+ kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ng’ombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.
16 “‘Ngati akupereka lonjezo+ monga nsembe yake kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo angathenso kudya imene yatsala pa tsiku lotsatira.
21 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake+ kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ng’ombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.