Numeri 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anawerenga kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse amene analowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako.+ Numeri 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Onse owerengedwa, malinga ndi mabanja awo, anakwana 2,750.+
35 Anawerenga kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse amene analowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako.+