Numeri 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma ngati mkaziyo ali wokwatiwa, ndipo akuchita lonjezo mwa kulumbirira moyo wake,+ kapena kulonjeza ndi pakamwa pake mosaganizira bwino, Numeri 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Komabe, ngati mkazi walonjeza ali m’nyumba ya mwamuna wake, kapena ngati wachita lonjezo lodzimana+ mwa kulumbirira moyo wake,
6 “Koma ngati mkaziyo ali wokwatiwa, ndipo akuchita lonjezo mwa kulumbirira moyo wake,+ kapena kulonjeza ndi pakamwa pake mosaganizira bwino,
10 “Komabe, ngati mkazi walonjeza ali m’nyumba ya mwamuna wake, kapena ngati wachita lonjezo lodzimana+ mwa kulumbirira moyo wake,