Ekisodo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo ana aamuna a Uziyeli anali Misayeli, Elizafana ndi Sitiri.+ 1 Mbiri 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana a Kohati+ anali Amuramu,+ Izara, Heburoni, ndi Uziyeli.+