-
Yoswa 1:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako, Yoswa analankhula ku fuko la Rubeni, ku fuko la Gadi, ndi ku hafu ya fuko la Manase, kuti:
-
-
Yoswa 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Akazi anu ndi ana anu aang’ono atsale limodzi ndi ziweto zanu m’dziko lino limene Mose anakupatsani, tsidya lino la Yorodano.+ Koma amunanu, mudzawoloka patsogolo pa abale anu, mutafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+ Inuyo, amuna nonse amphamvu ndi olimba mtima,+ muwoloke kuti mukawathandize abale anu.
-