Numeri 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Koma ngati mwachita cholakwa cholephera kusunga malamulo onsewa+ amene Yehova walankhula kudzera mwa Mose, Yakobo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero, ngati munthu akudziwa kuchita chabwino koma sakuchichita,+ akuchimwa.+
22 “‘Koma ngati mwachita cholakwa cholephera kusunga malamulo onsewa+ amene Yehova walankhula kudzera mwa Mose,