Yoswa 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Rubeni ndi ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase,+ anawoloka pamaso pa ana a Isiraeli atafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo,+ monga mmene Mose anawauzira.+
12 Ana a Rubeni ndi ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase,+ anawoloka pamaso pa ana a Isiraeli atafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo,+ monga mmene Mose anawauzira.+