Yoswa 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Malirewo analowera kum’mwera kuchitunda cha Akirabimu+ n’kukafika ku Zini.+ Kenako anakwera kuchokera kum’mwera kupita ku Kadesi-barinea,+ n’kukadutsa ku Hezironi mpaka ku Adara, n’kuzungulira kukafika ku Karika.
3 Malirewo analowera kum’mwera kuchitunda cha Akirabimu+ n’kukafika ku Zini.+ Kenako anakwera kuchokera kum’mwera kupita ku Kadesi-barinea,+ n’kukadutsa ku Hezironi mpaka ku Adara, n’kuzungulira kukafika ku Karika.