Numeri 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi dzina la bambo athu lichotsedwe ku banja lawo chifukwa chakuti analibe mwana wamwamuna?+ Chonde, tipatseni cholowa pakati pa abale awo a bambo athu.”+
4 Kodi dzina la bambo athu lichotsedwe ku banja lawo chifukwa chakuti analibe mwana wamwamuna?+ Chonde, tipatseni cholowa pakati pa abale awo a bambo athu.”+