Numeri 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zimene Yehova walamula zokhudza ana aakazi a Tselofekadi+ n’zakuti, ‘Iwo angakwatiwe ndi aliyense amene wawakomera m’maso. Koma akwatiwe ndi amuna a fuko la makolo awo okha.+
6 Zimene Yehova walamula zokhudza ana aakazi a Tselofekadi+ n’zakuti, ‘Iwo angakwatiwe ndi aliyense amene wawakomera m’maso. Koma akwatiwe ndi amuna a fuko la makolo awo okha.+