Numeri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+ Numeri 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Uwerenge ana onse a Gerisoni.+ Uwawerenge potsata nyumba za makolo awo malinga ndi mabanja awo.
15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+