Numeri 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mkazi wa munthu angazembere mwamuna wake n’kumuchimwira+ 1 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+
12 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mkazi wa munthu angazembere mwamuna wake n’kumuchimwira+
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+