Ezara 2:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+ Nehemiya 7:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Ndiyeno amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri,+ ndipo sanathe kufotokoza mzere wa makolo awo ndi kumene anachokera, kuti kaya anali ochokera mu Isiraeli kapena ayi, ndi awa:
62 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+
61 Ndiyeno amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri,+ ndipo sanathe kufotokoza mzere wa makolo awo ndi kumene anachokera, kuti kaya anali ochokera mu Isiraeli kapena ayi, ndi awa: