Ekisodo 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aliyense amene wawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita m’tsogolo azipereka choperekacho kwa Yehova.+ Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+
14 Aliyense amene wawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita m’tsogolo azipereka choperekacho kwa Yehova.+
29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+