Mlaliki 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pita ukadye chakudya chako mokondwera ndi kumwa vinyo wako ndi mtima wosangalala,+ chifukwa Mulungu woona wakondwera kale ndi ntchito zako.+ Mlaliki 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chakudya chimachititsa antchito kuseka, ndipo vinyo amachititsa moyo kusangalala,+ koma ndalama zimathandiza pa zinthu zonse.+
7 Pita ukadye chakudya chako mokondwera ndi kumwa vinyo wako ndi mtima wosangalala,+ chifukwa Mulungu woona wakondwera kale ndi ntchito zako.+
19 Chakudya chimachititsa antchito kuseka, ndipo vinyo amachititsa moyo kusangalala,+ koma ndalama zimathandiza pa zinthu zonse.+