Genesis 43:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yosefe atakweza maso ake n’kuona mng’ono wake Benjamini, m’bale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndiye mng’ono wanu amene munali kunena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima+ mwana wanga.”
29 Yosefe atakweza maso ake n’kuona mng’ono wake Benjamini, m’bale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndiye mng’ono wanu amene munali kunena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima+ mwana wanga.”