1 Mafumu 8:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Solomo anapereka nsembe zachiyanjano+ zimene anayenera kupereka kwa Yehova. Anapereka ng’ombe 22,000 ndi nkhosa 120,000+ kuti mfumuyo ndi ana onse a Isiraeli atsegulire+ nyumba ya Yehova. 2 Mbiri 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumu Solomo inapereka nsembe ya ng’ombe 22,000 ndi nkhosa 120,000.+ Choncho mfumuyo ndi anthu onse anatsegulira+ nyumba ya Mulungu woona.
63 Solomo anapereka nsembe zachiyanjano+ zimene anayenera kupereka kwa Yehova. Anapereka ng’ombe 22,000 ndi nkhosa 120,000+ kuti mfumuyo ndi ana onse a Isiraeli atsegulire+ nyumba ya Yehova.
5 Mfumu Solomo inapereka nsembe ya ng’ombe 22,000 ndi nkhosa 120,000.+ Choncho mfumuyo ndi anthu onse anatsegulira+ nyumba ya Mulungu woona.