Ekisodo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Upangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo uwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+ 1 Samueli 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Motero anthuwo anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa makamu, amene akukhala pa akerubi.+ Ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anali pamenepo ndi likasa la pangano la Mulungu woona.+ Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+
18 Upangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo uwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+
4 Motero anthuwo anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa makamu, amene akukhala pa akerubi.+ Ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anali pamenepo ndi likasa la pangano la Mulungu woona.+
80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+