Levitiko 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+ Aroma 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi. 2 Akorinto 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene analibe uchimoyo,+ Mulungu anamupanga kukhala uchimo+ chifukwa cha ife, kuti tikhale olungama pamaso pa Mulungu+ kudzera mwa iye.
3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+
3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi.
21 Amene analibe uchimoyo,+ Mulungu anamupanga kukhala uchimo+ chifukwa cha ife, kuti tikhale olungama pamaso pa Mulungu+ kudzera mwa iye.