Numeri 3:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana onse aamuna oyamba kubadwa a Isiraeli. Unditengerenso ziweto za Alevi zikhale zanga m’malo mwa ziweto za Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova.
45 “Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana onse aamuna oyamba kubadwa a Isiraeli. Unditengerenso ziweto za Alevi zikhale zanga m’malo mwa ziweto za Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova.