Ekisodo 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Mulungu anati: “Ineyo ndidzayenda nawe+ ndipo ndidzakupatsa mpumulo.”+ Ekisodo 40:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma ukapanda kukwera, iwo sanali kunyamuka mpaka tsiku limene wakwera.+