Ekisodo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo khamu lonse la ana a Isiraeli linanyamuka kuchipululu cha Sini.+ Ulendowo anaugawa mitundamitunda, malinga ndi mmene Yehova anawauzira,+ ndipo anamanga msasa wawo pa Refidimu.+ Koma pamenepo panalibe madzi akumwa. Numeri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anasamuka malinga ndi malangizo amene Yehova anapereka kudzera kwa Mose.+ Kameneka kanali koyamba kuti iwo asamuke.
17 Ndipo khamu lonse la ana a Isiraeli linanyamuka kuchipululu cha Sini.+ Ulendowo anaugawa mitundamitunda, malinga ndi mmene Yehova anawauzira,+ ndipo anamanga msasa wawo pa Refidimu.+ Koma pamenepo panalibe madzi akumwa.
13 Iwo anasamuka malinga ndi malangizo amene Yehova anapereka kudzera kwa Mose.+ Kameneka kanali koyamba kuti iwo asamuke.