Ekisodo 39:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a Isiraeli anachita utumiki wonse motsatira zonse zimene Yehova analamulira Mose.+