Numeri 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mose anatumiza amunawo kunkhondo, amuna 1,000 pa fuko lililonse. Anawatumiza limodzi ndi Pinihasi,+ mwana wa wansembe Eleazara. Pinihasi ananyamula ziwiya zopatulika ndi malipenga+ operekera zizindikiro. 1 Mbiri 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya, ndi Eliezere, anali ansembe omwe anali kuimba malipenga mokweza+ patsogolo pa likasa la Mulungu woona. Obedi-edomu ndi Yehiya anali alonda a Likasa. 1 Mbiri 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Benaya ndi Yahazieli, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga+ nthawi zonse patsogolo pa likasa la pangano la Mulungu woona. 2 Mbiri 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Aleviwo anaimirirabe atanyamula zipangizo zoimbira+ za Davide. Iwo anaimirira pamodzi ndi ansembe omwe ananyamula malipenga.+ Nehemiya 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mwa ana a ansembe oimba malipenga+ panalinso Zekariya mwana wa Yonatani. Yonatani anali mwana wa Semaya, Semaya anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali mwana wa Mikaya, Mikaya anali mwana wa Zakuri,+ ndipo Zakuri anali mwana wa Asafu.+ Nehemiya 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Kunafikanso ansembe otsatirawa okhala ndi malipenga:+ Eliyakimu, Maaseya, Miniyamini, Mikaya, Elioenai, Zekariya, Hananiya,
6 Ndiyeno Mose anatumiza amunawo kunkhondo, amuna 1,000 pa fuko lililonse. Anawatumiza limodzi ndi Pinihasi,+ mwana wa wansembe Eleazara. Pinihasi ananyamula ziwiya zopatulika ndi malipenga+ operekera zizindikiro.
24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya, ndi Eliezere, anali ansembe omwe anali kuimba malipenga mokweza+ patsogolo pa likasa la Mulungu woona. Obedi-edomu ndi Yehiya anali alonda a Likasa.
6 Benaya ndi Yahazieli, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga+ nthawi zonse patsogolo pa likasa la pangano la Mulungu woona.
26 Choncho Aleviwo anaimirirabe atanyamula zipangizo zoimbira+ za Davide. Iwo anaimirira pamodzi ndi ansembe omwe ananyamula malipenga.+
35 Mwa ana a ansembe oimba malipenga+ panalinso Zekariya mwana wa Yonatani. Yonatani anali mwana wa Semaya, Semaya anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali mwana wa Mikaya, Mikaya anali mwana wa Zakuri,+ ndipo Zakuri anali mwana wa Asafu.+
41 Kunafikanso ansembe otsatirawa okhala ndi malipenga:+ Eliyakimu, Maaseya, Miniyamini, Mikaya, Elioenai, Zekariya, Hananiya,