Numeri 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Efuraimu alipo 108,100. Amenewa azikhala achitatu kunyamuka.+
24 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Efuraimu alipo 108,100. Amenewa azikhala achitatu kunyamuka.+