Numeri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa ana a Yosefe+ kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase,+ Gamaliyeli mwana wa Pedazuri, Numeri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chigawo cha mafuko atatu cha Efuraimu+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumadzulo. Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi.
10 Mwa ana a Yosefe+ kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase,+ Gamaliyeli mwana wa Pedazuri,
18 “Chigawo cha mafuko atatu cha Efuraimu+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumadzulo. Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi.