Deuteronomo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Kuwonjezera apo, pa Tabera,+ pa Masa+ ndi pa Kibiroti-hatava+ munaputanso mkwiyo wa Yehova.+