Ekisodo 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero nyumba ya Isiraeli inayamba kutcha chakudyacho kuti “mana.”* Chinali choyera ngati njere ya mapira,* ndipo kukoma kwake kunali ngati makeke opyapyala othira uchi.+
31 Chotero nyumba ya Isiraeli inayamba kutcha chakudyacho kuti “mana.”* Chinali choyera ngati njere ya mapira,* ndipo kukoma kwake kunali ngati makeke opyapyala othira uchi.+