Yobu 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akunyansidwa nane, ndipo akukhala patali ndi ine.+Sakuzengereza kundilavulira kumaso.+ Yesaya 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Msana wanga ndinaupereka kwa ondimenya, ndipo masaya anga+ ndinawapereka kwa ozula ndevu. Nkhope yanga sindinaitchinjirize kuti isachitidwe zinthu zamanyazi ndi kulavuliridwa.+
6 Msana wanga ndinaupereka kwa ondimenya, ndipo masaya anga+ ndinawapereka kwa ozula ndevu. Nkhope yanga sindinaitchinjirize kuti isachitidwe zinthu zamanyazi ndi kulavuliridwa.+