Ekisodo 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero Mose anafuulira Yehova kuti: “Nditani nawo anthuwa? Angotsala pang’ono kundiponya miyala!”+
4 Chotero Mose anafuulira Yehova kuti: “Nditani nawo anthuwa? Angotsala pang’ono kundiponya miyala!”+