Numeri 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+ Numeri 26:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Zinakhala choncho chifukwa ponena za iwo, Yehova anati: “Mulimonsemo adzafera m’chipululu basi.”+ Choncho, sipanatsale ndi mmodzi yemwe kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+
65 Zinakhala choncho chifukwa ponena za iwo, Yehova anati: “Mulimonsemo adzafera m’chipululu basi.”+ Choncho, sipanatsale ndi mmodzi yemwe kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+